Nation Of 1

Текст песни Malawi Native Anthem Text

Malawi Native Anthem Text видео клип

No photo
Обзор
Голоса:
0
Смотри также:
Неверный текст?

Nation Of 1 - Текст песни Malawi Native Anthem Text

1.
Mlungu dalitsani Malawi,
Mumsunge m'mtendere.
Gonjetsani adani onse,
Njala, nthenda, nsanje.
Lunzitsani mitima yathu,
Kuti tisaope.
Mdalitse Mtsogo leri na fe,
Ndi Mai Malawi.
2.
Malawi ndziko lokongola,
La chonde ndi ufulu,
Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri,
Ndithudi tadala.Nation Of 1 - Malawi Native Anthem Text - http://ru.motolyrics.com/nation-of-1/malawi-native-anthem-text-lyrics.html
Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu,
N'mphatso zaulere.
Nkhalango, madambo abwino.
Ngwokoma Malawi.
3.
O! Ufulu tigwirizane,
Kukweza Malawi.
Ndi chikondi, khama, kumvera,
Timutumikire.
Pa nkhondo nkana pa mtendere,
Cholinga n'chimodzi.
Mai, bambo, tidzipereke,
Pokweza Malawi.
Sent by Carlos Andr? Pereira da Silva Branco

Оставить комментарий

Что вы думаете о песне "Malawi Native Anthem Text"? Напишите ваш комментарий.

Тексты песен альбома "Other Songs A - MAL"

Рекомендуемые песни